Mon Dec 06 2021 20:32:52 GMT+0000 (Greenwich Mean Time)

This commit is contained in:
tsDesktop 2021-12-06 20:32:52 +00:00
parent d90e9cf7a9
commit d01bd3aca0
3 changed files with 3 additions and 4 deletions

View File

@ -1 +1 @@
\v 6 Mfumu Yerobiamu anayanka nakukamba kuli munthu wa Mulungu ati, "Pempa kuti Yehova Mulungu wako ankale nau bwino ndipo unipempelele, kuti kwanja yanga ibwelele kuli ine." Kapolo wa Mulungu anapempela kuli Yehova, ndipo kwanja ya mfumu inabwezewa kuli eve, ndipo chinankala monga poyamba. \v 7 Mfumu inauza kapolo wa Mulungu uja, "bwela kunyumba naine ukapumule, ndipo nizakupasa mphsao."
\v 6 Mfumu Yerobiamu anayanka nakukamba kuli munthu wa Mulungu ati, "Pempa kuti Yehova Mulungu wako ankale nau bwino ndipo unipempelele, kuti kwanja yanga ibwelele kuli ine." Kapolo wa Mulungu anapempela kuli Yehova, ndipo kwanja ya mfumu inabwezewa kuli eve, ndipo chinankala monga poyamba. \v 7 Mfumu inauza kapolo wa Mulungu uja, "bwela kunyumba naine ukapumule, ndipo nizakupasa mphaso."

View File

@ -1 +1 @@
\v 8 Munthu wa Mulungu anati kwa mfumu, "Ngakhale utandipatsa theka la chuma chako, sindipita nawe, kapena kudya kapena kumwa madzi pamalo ano, \v 9 chifukwa Yehova anandilamula mwa mawu ake kuti, 'Udye osatenga mkate kapena kumwa madzi, kapena kubwerera panjira imene wabwerera.” \v 10 Munthu wa Mulungu woonayo anachoka njira ina ndipo sanabwerere kunyumba kwake kudzera njira imene anapita ku Beteli.
\v 8 Kapolo wa Mulungu ana kwa mfumu, "Ngakhale utandipatsa theka la chuma chako, sindipita nawe, kapena kudya kapena kumwa madzi pamalo ano, \v 9 chifukwa Yehova anandilamula mwa mawu ake kuti, 'Udye osatenga mkate kapena kumwa madzi, kapena kubwerera panjira imene wabwerera.” \v 10 Munthu wa Mulungu woonayo anachoka njira ina ndipo sanabwerere kunyumba kwake kudzera njira imene anapita ku Beteli.

View File

@ -261,13 +261,12 @@
"13-title",
"13-01",
"13-04",
"13-08",
"13-06",
"13-11",
"13-14",
"13-18",
"13-20",
"13-23",
"13-26",
"13-29",
"13-31",
"13-33",