Sat Apr 20 2024 10:01:10 GMT+0200 (South Africa Standard Time)

This commit is contained in:
Timothy Muzgatama 2024-04-20 10:01:13 +02:00
parent ad6b9fa6e3
commit c0f9861342
4 changed files with 4 additions and 1 deletions

View File

@ -1 +1 @@
\v 39 \v 40 Nkhani zina zokhudza Ahabu ndi zonse zimene anachita, nyumba ya minyanga ya njovu imene anamanga ndi mizinda yonse imene anamanga, zinalembedwa mbuku la zochitika za mafumu a Isiraeli kodi? Choncho Ahabu anagona pamodzi ndi makolo ake, ndipo Ahaziya mwana wake anayamba kulamulira mmalo mwake.
\v 39 Nkhani zina zokhudza Ahabu ndi zonse zimene anachita, nyumba ya minyanga ya njovu imene anamanga ndi mizinda yonse imene anamanga, zinalembedwa mbuku la zochitika za mafumu a Isiraeli kodi? \v 40 Choncho Ahabu anagona pamodzi ndi makolo ake, ndipo Ahaziya mwana wake anayamba kulamulira mmalo mwake.

1
22/41.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 41 Kenako Yehosafati mwana wa Asa anayamba kulamulira Yuda mchaka chachinayi cha Ahabu mfumu ya Isiraeli. \v 42 Yehosafati anali wa zaka makumi atatu kudza zisanu polowa ufumu wace, nakhala mfumu m'Yerusalemu zaka makumi awiri mphambu zisanu. Dzina la amayi ake linali Azuba mwana wa Sili.

1
22/43.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 43 Iye anayenda mnjira za atate wake Asa; sanapatuke kwa iwo; Iye anachita zoyenera pamaso pa Yehova. Koma misanje sinachotsedwe. Anthu anali kuperekabe nsembe ndi kufukiza pamisanje. \v 44 Yehosafati anachita mtendere ndi mfumu ya Isiraeli.

View File

@ -414,6 +414,7 @@
"22-34",
"22-35",
"22-37",
"22-39",
"22-41",
"22-43",
"22-45",