diff --git a/22/48.txt b/22/48.txt index 002eacc..74fd43e 100644 --- a/22/48.txt +++ b/22/48.txt @@ -1 +1 @@ -Yehosafati anamanga zombo za ku Tarisi; Anayenera kupita ku Ofiri kukatenga golide, koma sanapite chifukwa zombozo zinasweka ku Ezioni Geberi. Pamenepo Ahaziya mwana wa Ahabu anauza Yehosafati kuti: “Atumiki anga apite limodzi ndi atumiki ako m’zombo. Koma Yehosafati sanalole. Yehosafati anagona pamodzi ndi makolo ake, naikidwa pamodzi ndi makolo ake mu Mzinda wa Davide kholo lake; Yehoramu mwana wake anakhala mfumu m’malo mwake. \ No newline at end of file +\v 48 Yehosafati anamanga zombo za ku Tarisi; Anayenera kupita ku Ofiri kukatenga golide, koma sanapite chifukwa zombozo zinasweka ku Ezioni Geberi. \v 49 Pamenepo Ahaziya mwana wa Ahabu anauza Yehosafati kuti: “Atumiki anga apite limodzi ndi atumiki ako m’zombo. Koma Yehosafati sanalole. \v 50 Yehosafati anagona pamodzi ndi makolo ake, naikidwa pamodzi ndi makolo ake mu Mzinda wa Davide kholo lake; Yehoramu mwana wake anakhala mfumu m’malo mwake. \ No newline at end of file diff --git a/22/51.txt b/22/51.txt new file mode 100644 index 0000000..605e59b --- /dev/null +++ b/22/51.txt @@ -0,0 +1 @@ +\v 51 Ahaziya mwana wa Ahabu anakhala mfumu ya Isiraeli ku Samariya m’chaka cha 17 cha Yehosafati mfumu ya Yuda, ndipo analamulira Isiraeli zaka ziwiri. \v 52 Iye anachita zoipa pamaso pa Yehova, ndipo anayenda m’njira ya bambo ake, m’njira ya mayi ake, ndi m’njira ya Yerobiamu mwana wa Nebati, imene anachimwitsa nayo Isiraeli. \v 53 Iye anatumikira Baala ndi kum’lambira, moti anakwiyitsa Yehova Mulungu wa Isiraeli, monga mmene bambo ake anachitira. \ No newline at end of file diff --git a/manifest.json b/manifest.json index 24b90ff..1e432de 100644 --- a/manifest.json +++ b/manifest.json @@ -418,6 +418,7 @@ "22-41", "22-43", "22-45", + "22-48", "22-51" ] } \ No newline at end of file