From 95565ff3783ddb0e3f11cde61a4f29f8be7f217c Mon Sep 17 00:00:00 2001 From: Muzgatama Date: Thu, 18 Apr 2024 15:27:06 +0200 Subject: [PATCH] Thu Apr 18 2024 15:27:04 GMT+0200 (South Africa Standard Time) --- 09/24.txt | 1 + 09/25.txt | 1 + 09/26.txt | 1 + 10/01.txt | 1 + 10/title.txt | 1 + manifest.json | 2 +- 6 files changed, 6 insertions(+), 1 deletion(-) create mode 100644 09/24.txt create mode 100644 09/25.txt create mode 100644 09/26.txt create mode 100644 10/01.txt create mode 100644 10/title.txt diff --git a/09/24.txt b/09/24.txt new file mode 100644 index 0000000..a7071c8 --- /dev/null +++ b/09/24.txt @@ -0,0 +1 @@ +\v 24 Mwana wamkazi wa Farao anachoka mumzinda wa Davide n’kupita ku nyumba imene Solomo anam’mangira. Pambuyo pake, Solomo anamanga Milo. \ No newline at end of file diff --git a/09/25.txt b/09/25.txt new file mode 100644 index 0000000..3466732 --- /dev/null +++ b/09/25.txt @@ -0,0 +1 @@ +\v 25 Katatu caka ciliconse Solomo anali kupeleka nsembe zopsereza ndi zaciyanjano pa guwa lansembe limene anamangira Yehova, nafukiza nazo zofukiza pa guwa lansembe limene linali pamaso pa Yehova. Chotero anamaliza kachisi ndipo tsopano anali kuligwiritsa ntchito. \ No newline at end of file diff --git a/09/26.txt b/09/26.txt new file mode 100644 index 0000000..002fdad --- /dev/null +++ b/09/26.txt @@ -0,0 +1 @@ +\v 26 Mfumu Solomo inamanga zombo zankhondo ku Ezioni Geberi, pafupi ndi Elati m’mphepete mwa Nyanja Yofiira m’dziko la Edomu. \v 27 Hiramu anatumiza atumiki ku zombo za Solomo, amalinyero odziwa bwino nyanja, pamodzi ndi antchito a Solomo. \v 28 Iwo anapita ku Ofiri pamodzi ndi atumiki a Solomo. Kumeneko anabweretsa matalente 420 agolide kwa Mfumu Solomo. \ No newline at end of file diff --git a/10/01.txt b/10/01.txt new file mode 100644 index 0000000..64e0750 --- /dev/null +++ b/10/01.txt @@ -0,0 +1 @@ +\c 10 \v 1 Mfumu yaikazi ya ku Sheba itamva za Solomo za dzina la Yehova, inadza kudzamuyesa ndi mafunso ovuta. \v 2 Iye anafika ku Yerusalemu ndi gulu lalitali kwambiri, ngamila zonyamula zonunkhira, golide wambiri, ndi miyala yamtengo wapatali. Atafika, anauza Solomo zonse zimene zinali mumtima mwake. \ No newline at end of file diff --git a/10/title.txt b/10/title.txt new file mode 100644 index 0000000..9242427 --- /dev/null +++ b/10/title.txt @@ -0,0 +1 @@ +Mutu 10 \ No newline at end of file diff --git a/manifest.json b/manifest.json index b9aacf9..13d05a0 100644 --- a/manifest.json +++ b/manifest.json @@ -206,11 +206,11 @@ "09-17", "09-20", "09-22", + "09-23", "09-24", "09-25", "09-26", "10-title", - "10-01", "10-03", "10-06", "10-08",