Thu Apr 18 2024 15:35:06 GMT+0200 (South Africa Standard Time)

This commit is contained in:
Timothy Muzgatama 2024-04-18 15:35:07 +02:00
parent f21931b50d
commit 672f56f30b
3 changed files with 3 additions and 0 deletions

1
10/16.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 16 Mfumu Solomo inapanga zishango zazikulu mazana awiri zagolide wosakaniza ndi zitsulo zina. Masekeli mazana asanu ndi limodzi a golidi analowa m'modzi. \v 17 Anapanganso zishango mazana atatu zagolide wosakaniza ndi zitsulo zina. chishango chilichonse chinali ndi mamina atatu agolidi; mfumu inawaika mnyumba ya mfumu ya Nkhalango ya Lebanoni.

1
10/18.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 18 Kenako mfumu inapanga mpando waukulu wa minyanga ya njovu nkuukuta ndi golide woyengeka bwino. \v 19 Panali masitepe 6 opita kumpando wachifumuwo, ndipo nsonga yake inali yozungulira kumbuyo kwake. Kumbali zonse za mpandowo kunali zoikiramo manja, ndi mikango iwiri itaimirira mmbali mwa mawondowo. \v 20 Mikango khumi ndi iwiri inayimirira pamakwerero, imodzi mbali iyi ndi imodzi ya makwerero asanu ndi limodzi. Panalibe mpando wachifumu wonga umenewo mu ufumu wina uliwonse.

1
10/21.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 21 Zikho zonse zomweramo Mfumu Solomo zinali zagolide, ndi zikho zonse zomweramo za mNkhalango ya Lebanoni zinali zagolide woyenga bwino. Panalibe siliva, chifukwa siliva sanali wofunika mmasiku a Solomo. \v 22 Mfumuyo inali ndi zombo za ku Tarisi panyanja pamodzi ndi gulu la Hiramu. Zombozo zinkabwera ndi golidi, siliva, minyanga ya njovu kamodzi pa zaka zitatu zilizonse, anyani ndi anyani.