Thu Apr 18 2024 15:23:05 GMT+0200 (South Africa Standard Time)
This commit is contained in:
parent
ac6388268a
commit
109ca23e16
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 10 Ndipo kunali, pakutha zaka makumi awiri, Solomo anatsiriza kumanga nyumba ziwirizo, Kacisi wa Yehova ndi nyumba ya mfumu. \v 11 Tsopano Hiramu mfumu ya Turo anapatsa Solomo mitengo ya mkungudza ndi mikungudza, ndi golidi, zonse zimene Solomo anafuna, motero Mfumu Solomo inapatsa Hiramu mizinda 20 m’dziko la Galileya.
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 12 Hiramu anaturuka ku Turo kukaona midzi imene Solomo anampatsa, koma sanamkomera. \v 13 Ndipo Hiramu anati, Ndi midzi yotani iyi wandipatsa ine, mbale wanga? Hiramu anawatcha Dziko la Kabul, limene amalitchulabe mpaka pano. \v 14 Hiramu anatumiza kwa mfumu matalente 120 agolide.
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 15 Izi ndi nkhani za anthu okakamiza amene Mfumu Solomo analamula kuti amange kachisi wa Yehova ndi nyumba yake yachifumu, Milo, linga la Yerusalemu, Hazori, Megido, ndi Gezeri. \v 16 Farao mfumu ya Aigupto anakwera nalanda Gezeri. Anautentha ndi kupha Akanani a mumzindawo. Kenako Farao anapereka mzindawu kwa mwana wake wamkazi, mkazi wa Solomo, monga mphatso ya ukwati.
|
Loading…
Reference in New Issue