Thu Oct 07 2021 11:01:12 GMT+0200 (Central Africa Time)

This commit is contained in:
tsDesktop 2021-10-07 11:01:12 +02:00
parent 42971b2fdd
commit db7a22fca0
4 changed files with 8 additions and 1 deletions

1
17/22.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 22 Inu munapanga Israyeli kukhala anthu anu nthawi zonse, ndipo inu Yehova munakhala Mulungu wao. \v 23 Cifukwa cace tsono, Yehova, lonjezano lanu lokhudza mtumiki wanu ndi banja lace likhazikike kosatha. Chitani monga mwanenera. \v 24 Dzina lanu likhazikike kwamuyaya ndi kukhala wamkulu, kotero anthu adzati, 'Yehova wa makamu ndiye Mulungu wa Israeli,' pamene nyumba yanga, Davide mtumiki wanu yakhazikika pamaso panu.

1
17/25.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 25 Pakuti inu Mulungu wanga mwaulula kwa ine mtumiki wanu kuti mudzamumangira nyumba. N whychifukwa chake ine mtumiki wanu ndapeza kulimbika kwa kupemphera kwa inu. \v 26 Tsopano, Yehova, Inu ndinu Mulungu, ndipo mwapangana ndi lonjezo labwino ili kwa ine mtumiki wanu: \v 27 Tsopano chikukondweretsani inu kudalitsa nyumba ya kapolo wanu, kuti ikhale chikhalire pamaso panu. Inu, Yehova, mudalitsadi, ndipo idzadalitsidwa kosatha. "

1
18/title.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
Mutu 18

View File

@ -286,6 +286,10 @@
"17-09",
"17-11",
"17-13",
"17-16"
"17-16",
"17-19",
"17-22",
"17-25",
"18-title"
]
}