Thu Oct 07 2021 12:35:36 GMT+0200 (Central Africa Time)

This commit is contained in:
tsDesktop 2021-10-07 12:35:36 +02:00
parent 440c57f772
commit cc0a482251
5 changed files with 8 additions and 1 deletions

1
26/29.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 29 Pa zidzukulu za Izara, Kenaniya ndi ana ake aamuna anali oyang'anira zochitika za m civildziko la Israeli. Iwo anali akapitawo ndi oweruza. \v 30 Pa zidzukulu za Heburoni, Hasabiya ndi abale ake, amuna oyenerera okwanira 1,700, ankayang workanira ntchito ya Yehova ndi ntchito ya mfumu. Iwo anali kumadzulo kwa Yordano.

1
26/31.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 31 Kuchokera ku zidzukulu za Hebroni, Yeriya anali mtsogoleri wa zidzukulu zake, owerengedwa mwa mndandanda wa mabanja awo. M'chaka cha 40 cha ulamuliro wa Davide, iwo anafufuza m'mabuku a mbiri yawo ndipo anapeza ena mwa amuna odziwa bwino ntchito yawo ku Yazeri wa ku Giliyadi. \v 32 Yeriya anali ndi achibale 2,700, omwe anali atsogoleri othandiza mabanja. Davide anawayika akhale oyang'anira a fuko la Rubeni, Gadi, ndi theka la fuko la Manase, pa ntchito zonse za Mulungu ndi ntchito za mfumu.

1
27/01.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\c 27 \v 1 Ili ndilo mndandanda wa atsogoleri a mabanja a Israeli, atsogoleri a magulu a anthu 1,000, ndi atsogoleri a ankhondo amene ankatumikira mfumu m'njira zosiyanasiyana. Magulu onse ankhondo anali kugwira ntchito mwezi ndi mwezi chaka chonse. \v 2 Chigawo chilichonse chinali ndi amuna 24,000. Mtsogoleri wa gulu loyamba, la mwezi woyamba, anali Yashobeamu mwana wa Zabidieli. Gulu lake linali amuna 24,000. + \v 3 Iye anali mmodzi mwa ana a Perezi + komanso anali mtsogoleri wa atsogoleri onse a gulu la nkhondo pamwezi woyamba.

1
27/title.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
Mutu 27

View File

@ -380,6 +380,9 @@
"26-17",
"26-20",
"26-23",
"26-26"
"26-26",
"26-29",
"26-31",
"27-title"
]
}