Thu Oct 07 2021 11:37:18 GMT+0200 (Central Africa Time)

This commit is contained in:
tsDesktop 2021-10-07 11:37:18 +02:00
parent dc58078a40
commit c5dee1897a
5 changed files with 9 additions and 2 deletions

View File

@ -1 +1 @@
\v 30 \v 31 Iwo ankayimiranso m'mawa uliwonse kuthokoza ndi kutamanda Yehova. Ankachitanso zimenezi madzulo ndi nthawi iliyonse yopereka nsembe zopsereza kwa Yehova, pa Sabata ndi pa zikondwerero za mwezi watsopano ndi masiku a maphwando. Chiwerengero chokhazikika, choperekedwa ndi lamulo, nthawi zonse chimayenera kupezeka pamaso pa Yehova.
\v 30 Iwo ankayimiranso m'mawa uliwonse kuthokoza ndi kutamanda Yehova. Ankachitanso zimenezi madzulo \v 31 ndi nthawi iliyonse yopereka nsembe zopsereza kwa Yehova, pa Sabata ndi pa zikondwerero za mwezi watsopano ndi masiku a maphwando. Chiwerengero chokhazikika, choperekedwa ndi lamulo, nthawi zonse chimayenera kupezeka pamaso pa Yehova.

1
23/32.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 32 Iwo anali kuyang'anira chihema chokumanako, malo oyera, ndipo anali kuthandiza abale awo a Aroni potumikira m'nyumba ya Yehova.

1
24/01.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\c 24 \v 1 Magulu a anthu ogwira ntchito motsatira zidzukulu za Aaroni anali awa: \v 2 Nadabu, Abihu, Eleazara ndi Itamara. Nadabu ndi Abihu anamwalira abambo awo asanamwalire. Analibe ana, choncho Eleazara ndi Itamara anali ansembe. \v 3 Davide pamodzi ndi Zadoki, mbadwa ya Eleazara, ndi Ahimeleki, mbadwa ya Itamara, anawagawa mmagulu kuti azigwira ntchito yawo yaunsembe.

1
24/title.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
Mutu 24

View File

@ -345,6 +345,10 @@
"23-19",
"23-21",
"23-24",
"23-27"
"23-27",
"23-30",
"23-32",
"24-title",
"24-01"
]
}