Thu Oct 07 2021 10:49:11 GMT+0200 (Central Africa Time)

This commit is contained in:
tsDesktop 2021-10-07 10:49:11 +02:00
parent fd0dc2c5ce
commit b74d18e112
6 changed files with 11 additions and 1 deletions

1
16/37.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 37 Kotero Davide anasiya Asafu ndi abale ake kumeneko patsogolo pa Bokosi la Chipangano la Yehova, kuti azitumikira mosalekeza patsogolo pa Likasa, monga mwa ntchito za tsiku ndi tsiku. \v 38 Obedi Edomu ndi abale awo makumi asanu ndi limodzi mphambu asanu ndi atatu anaphatikizidwa. Obedi Edomu mwana wa Yedutuni, pamodzi ndi Hosa anali odikira. \v 39 Wansembe Zadoki ndi ansembe anzake anatumikira patsogolo pa chihema cha Yehova ku malo okwezeka a ku Gibeoni.

1
16/40.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 40 Anali kupereka nsembe zopsereza kwa Yehova paguwa lansembe zopsereza mosalekeza m'mawa ndi madzulo, mogwirizana ndi zonse zolembedwa m lawchilamulo cha Yehova, chimene analamula Israeli. \v 41 Hemani ndi Yedutuni anali nawo, pamodzi ndi enawo amene anasankhidwa ndi mayina, kuti ayamike Yehova; chifukwa chake pangano lake ndi la chikhalire.

1
16/42.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 42 Hemani ndi Yedutuni anali oyang'anira oyimba malipenga, zinganga ndi zida zina zoyimbira Mulungu. Ana a Yedutuni anali olondera pachipata. \v 43 Pamenepo anthu onse anabwerera kunyumba zawo, ndipo Davide anabwerera kudalitsa banja lake.

1
17/01.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\c 17 \v 1 Ndipo panali atakhala mfumu m'nyumba mwace, anati kwa Natani mneneriyo, Tawonani, ine ndikhala m'nyumba ya mkungudza, koma likasa la cipangano la Yehova likhalabe pansi pa hema. \v 2 Natani anati kwa Davide, "Pita, kachita zomwe zili mumtima mwako, chifukwa Mulungu ali ndi iwe."

1
17/title.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
Mutu 17

View File

@ -275,6 +275,11 @@
"16-30",
"16-32",
"16-34",
"16-36"
"16-36",
"16-37",
"16-40",
"16-42",
"17-title",
"17-01"
]
}