Thu Oct 07 2021 12:43:37 GMT+0200 (Central Africa Time)

This commit is contained in:
tsDesktop 2021-10-07 12:43:37 +02:00
parent 4186deafc6
commit 8409e8e2ef
6 changed files with 11 additions and 1 deletions

1
27/28.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 28 Baala-Hanani wa ku Gederi anali kuyang'anira mitengo ya maolivi ndi mitengo ya mkuyu yomwe inali kuchigwa. \v 29 Oyang'anira zoweta zoweta m'Sharoni anali Shitrai wa ku Sharoni, ndi woyang'anira zoweta zomwe zinali m'zigwa anali Safati mwana wa Adlai.

1
27/30.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 30 Woyang'anira ngamila anali Obili Mwisimaeli, woyang'anira abulu aakazi anali Yedeya wa ku Meronoti. Woyang'anira nkhosa anali Yazizi Mhagara. \v 31 Yazizi wa ku Hagara anali woyang'anira gulu la ziweto. Atsogoleri onsewa anali oyang'anira katundu wa Mfumu Davide.

1
27/32.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 32 Yonatani, amalume ake a Davide, anali mlangizi, chifukwa anali munthu wanzeru komanso mlembi. Yehieli mwana wa Hakimoni anayang'anira ana aamuna a mfumu. \v 33 Ahitofeli anali mlangizi wa mfumu, ndipo Hushai wa Aariki anali mthandizi wa mfumu paokha. \v 34 Ahitofeli anatenga udindo wa Yehoyada mwana wa Benaya ndi Abiyatara. Yowabu anali mtsogoleri wa ankhondo.

1
28/01.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\c 28 \v 1 Davide anasonkhanitsa akalonga onse a Israeli ku Yerusalemu: atsogoleri a mafuko, oyang ofanira magulu amene anali kutumikira mfumu pa ntchito yawo, atsogoleri a magulu a anthu 1,000 ndi a anthu 100, oyang overanira katundu ndi katundu wa mfumu. mwa ana ake aamuna, ndi akapitawo, ndi amuna ankhondo, kuphatikizapo aluso koposa mwa iwo.

1
28/title.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
Mutu 28

View File

@ -392,6 +392,11 @@
"27-16",
"27-19",
"27-23",
"27-25"
"27-25",
"27-28",
"27-30",
"27-32",
"28-title",
"28-01"
]
}