Thu Oct 07 2021 11:53:28 GMT+0200 (Central Africa Time)

This commit is contained in:
tsDesktop 2021-10-07 11:53:28 +02:00
parent 6992f874e9
commit 66f12390ba
5 changed files with 9 additions and 1 deletions

1
24/29.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 29 Kuchokera kwa Kisi: Mwana wa Kisi anali Yerameeli. \v 30 Ana a Musi anali Mali, Ederi, ndi Yerimoti. Awa anali Alevi potsata mabanja awo. \v 31 Amuna onse amene anali atsogoleri a nyumba ya makolo ndi aliyense wa abale awo achichepere anachita maere pamaso pa Mfumu Davide, Zadoki ndi Ahimeleki, pamodzi ndi atsogoleri a mabanja a ansembe ndi Alevi. Iwo anachita maere monga anachitira ana a Aroni.

1
25/01.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\c 25 \v 1 Davide ndi atsogoleri a ankhondo anasankha ena mwa ana a Asafu, Hemani ndi Yedutuni kuti alosere ndi zingwe ndi azeze ndi zinganga. Uwu ndiwo mndandanda wa amuna amene anatumikira: \v 2 Kuchokera mwa ana a Asafu: Zakuri, Yosefe, Netaniya, ndi Asharela, ana a Asafu motsogozedwa ndi Asafu amene anali kunenera motsogozedwa ndi mfumu. \v 3 Kuchokera mwa ana a Yedutuni: Gedaliya, Zeri, Yeshaya, Simeyi, Hasabiya, ndi Matitiya. Onse pamodzi analamulidwa ndi bambo awo Yedutuni, amene anali kuimba zeze posonyeza kuyamikira ndi kutamanda Yehova

2
25/04.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1,2 @@
Kuchokera mwa ana a Hemani panali Bukiya, Mataniya, Uziyeli,
Shubaeli, Yerimoti, Hananiya, Hanani, Eliata, Gidalti, Romamti Ezeri, Yoshibekasha, Maloti, Hotiri ndi Mahazioti. Onsewa anali ana a Hemani mneneri wa mfumu. Mulungu anapatsa Hemani ana khumi ndi anayi ndi ana aakazi atatu kuti akweze nyanga yake.

1
25/title.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
Mutu 25

View File

@ -358,6 +358,9 @@
"24-19",
"24-20",
"24-23",
"24-26"
"24-26",
"24-29",
"25-title",
"25-01"
]
}