Thu Oct 07 2021 11:19:14 GMT+0200 (Central Africa Time)

This commit is contained in:
tsDesktop 2021-10-07 11:19:14 +02:00
parent 6349f38804
commit 47e50be762
6 changed files with 11 additions and 1 deletions

1
21/23.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 23 Orinani anati kwa Davide, "Dzitengereni nokha, mbuye wanga mfumu. Chitani chomwe chiri chabwino pamaso panu. Taonani, ndidzakupatsani ng'ombe za nsembe yopsereza, zopunthira matabwa, ndi tirigu wa nsembe yambewu; Ndikupatsani zonsezi. " \v 24 Mfumu Davide inauza Ornani, "Ayi, ndikulimbikira kuti ndigule pa mtengo wathunthu. Sindingatenge zanu zanu ndikupereka ngati nsembe yopsereza kwa Yehova ngati sizindilipira chilichonse."

1
21/25.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 25 Ndipo Davide analipira golidi mazana asanu ndi limodzi a malowo. \v 26 Davide anamangira Yehova guwa la nsembe kumeneko; naperekapo nsembe zopsereza, ndi nsembe zoyamika. Anaitana kwa Yehova, amene anamyankha ndi moto wochokera kumwamba pa guwa la nsembe yopsereza. \v 27 Kenako Yehova analamula mngeloyo, ndipo mngeloyo anabwezera lupanga lake m'chimake.

1
21/28.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 28 Davide ataona kuti Yehova wamuyankha pa malo opunthira mbewu a Orinani Myebusi, anapereka nsembe kumeneko nthawi yomweyo. \v 29 Tsopano pa nthawi imeneyo chihema cha Yehova, chimene Mose anachipanga m'chipululu, ndi guwa la nsembe yopsereza, zinali pa msanje pa Gibeoni. \v 30 Komabe, Davide sakanatha kupita kumeneko kukapempha chitsogozo cha Mulungu, chifukwa adaopa lupanga la mngelo wa Yehova.

1
22/01.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\c 22 \v 1 Ndipo Davide anati, Apa ndi pamene pali nyumba ya Yehova Mulungu, ndi guwa la nsembe zopsereza za Israyeli. \v 2 Ndipo Davide analamula anyamata ake kuti asonkhanitse alendo amene akukhala m ofdziko la Israeli. Anawaika kukhala odula miyala, kudula miyala, kuti amange nyumba ya Mulungu.

1
22/title.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
Mutu 22

View File

@ -322,6 +322,11 @@
"21-13",
"21-16",
"21-18",
"21-21"
"21-21",
"21-23",
"21-25",
"21-28",
"22-title",
"22-01"
]
}