ny_mrk_text_reg/07/24.txt

1 line
410 B
Plaintext

\v 24 Iye anacokako kuja ndi kupita ku Tire ndi ku Sidoni. Anangena mnyumba ndipo sanafune kuti anthu aone kuti anali muja, koma sanabisame. \v 25 Koma panthawi yamene iyo mzimai, amene anali ndi mwana mkazi wamene anali ndi mizimu yonyansa, anamva za iye, anabwela kwaiye ndi kugwa pa mendo yake. \v 26 Manje mzimai anali wa cigiriki, mtundu wa Msurofonika. Anamupempha kuti amucosele ciwanda mumwana wake.