2 lines
345 B
Plaintext
2 lines
345 B
Plaintext
\v 20 Iye anati, "Ni cija camene camene cicokela mkati inye camene cimadesa munthu.
|
|
\v 21 Cifukwa kucokela mkati mwa munthu, kucokela m'mtima, mcokela malingalilo woyipa, zaciwelewele, zaukawalala, zakupaya, \v 22 zacigololo, zokumbwa, zoipa, zacinyengo, kuzitukumula, zopusa. \v 23 Zonse izi zoipa zicokela mkati, ndiye zimene zimadesa munthu." |