ny_mrk_text_reg/07/02.txt

1 line
383 B
Plaintext

\v 2 Ndipo anaona kuti wophunzila ake ena analikudya ndi manja yodesedwa, amene yosasamba. \v 3 (Cifukwa Afalisi ndi Ayuda wonse sanalikudya wosasamba kumanja, cifukwa anagwililila kumwambo wa makolo. \v 4 Pamene Afalisi acokela ku msika, sanalikudya ngati sanasambe. ndipo kunali miyambo yambiri yamene sanafune kutaya, kuikapo ndi kusuka makapu, mapoto, viya ndi Tebulo yodyelapo.)