\v 57 Ena anabwelesa umboni waboza kumunenela; iwo anati, \v 58 "Tinamvela uyu munthu akunena kuti, 'Ndingagwese tempele iyi ndimanja yanga, ndipo m'masiku yatatu ndingamange ina yosamangika ndi manja." \v 59 Cukanga uyu umboni sunagwilizane.