\v 55 Manje mkulu wa ansembe ndi bungwe yonse ya Ayuda anali kufuna-funa umboni womususa Yesu kuti ampaye. Koma sanaupeze . \v 56 Cifukwa ambiri anabwela ndi umboni waboza kumunamizila iye, koma cukanga umboni wawo sunagwirizane.