ny_mrk_text_reg/14/53.txt

2 lines
244 B
Plaintext

\v 53 Anamsogolela Yesu kwa mkulu wansembe. Kwamene kuja anasonkhana naye akulu ansembe, akulu ndi alembi.
\v 54 Manje Petulo analikumsata iye patali, patali ngati nyumba ya mkulu wansembe. Anankhala pakati pa asilikali, amene anali kuota moto.