1 line
507 B
Plaintext
1 line
507 B
Plaintext
\v 12 Siku yoyamba ya buledi yopanda cotupisa, pamene anapeleka nkhosa nsembe ya pasaka, wophunzila ake anti kwa iye, "Mufuna kuti tiyende kuti tikhakonze, kuti tidye cakudya ca pasaka?" \v 13 Anatuma awiri wa wophunzira ake ndikunena nawo kuti, "Pitani kumzinda, mzakumana ndi munthu wonyamula mgomo wa manzi. M'mukonkhe iye. \v 14 Pamene azangena mnyumba, nainunso mngene ndipo muti kwa mwine nyumba kuti, 'Mphunzisi anti, "kodi cipinda canga ca alendo niciti kuti tidyelemo pasaka ndi wophunzira anga?" |