|
\v 35 Cifukwa aliyense amene kusunga moyo wake azautaya, ndi yense amene ataya moyo wake cifukwa ca uthenga wanga, azausunga. \v 36 Kodi cipindula bwanji ku munthu, kuthenga ziko yonse, ndi kutayamoyo wake? \v 37 Kodi munthu angacinjane nacani na umoyo wake? |