1 line
298 B
Plaintext
1 line
298 B
Plaintext
\v 31 Ndipo anayamba kuwaphunzisa kuti Mwana wa Munthu afunika kusausidwa pa zinthu zambiri, ndipo azakanidwa ndi azikulu ndi akulu ansembe ndi alembi, ndipo azapaiwa, koma pazapita masiku atatu azauka. \v 32 Analankula izi momveka bwino. Apo Petulo anamtenga iye pambali ndikuyamba kumuzuzula iye. |