ny_mrk_text_reg/08/18.txt

1 line
269 B
Plaintext

\v 18 Muli nawo menso, Kodi simuona? Muli nawo matu, Kodi simvela? kodi simukumbuka? \v 19 Pamene ndinanyema mitanda faivi ndikudyesa anthu faivi sauzande, ndi mabasiketi yangati yamene anazula ndi nyenswa zosala za buledi yamene munathenga?" Anati kwa iye, "Twelufu."