|
\v 16 Wophunzila anayamba kufusana wina ndi mzace, "Kodi ndicifukwa cakuti tilibe buledi." \v 17 Yesu anazidikila pali ici ndipo anati kwa iwo, "Kodi nicifukwa ciani muli kulingilila za buledi kuti mulibe? Kodi simunaziwe? Simunamvesese kodi? Kodi mitima yanu yaleka kuziwa? |