\v 14 Tsopano wophunzila anaiwala kunyamula buledi. Munali cabe mtanda umozi wa buledi m'boti. \v 15 Anawacenjeza iwo ndi kunena kuti, "Nkhalani celu ndipo woyanganila kususana ndi cizamba ca Afalisi ndi cizamba ca Herode."