ny_mrk_text_reg/08/07.txt

1 line
382 B
Plaintext

\v 7 Iwo anali ndi tisomba tung'ono ndipo pambuyo poyamika, analamulila wophunzira kuti agawiletso anthu. \v 8 Anadya ndipo anakutha. Ndipo anatheka nyenswa zosala, mabasiketi yakulu yali seveni. \v 9 Panali anthu wokwanila folo sauzande. Ndipo anawalola tsopano kuti apite. \v 10 Panthawi yamene yamene iyo, anangena m'boti ndi wophunzila ake, ndipo anayende ku cigawo ca Damanuta.