ny_mrk_text_reg/07/27.txt

1 line
239 B
Plaintext

\v 27 Iye anati kwa iye, "Leka ana adye coyamba. Cifukwa sicabwino kutenga buledi ya ana ndikuponyela agalu." \v 28 Koma iye anayankha nati kwa iye, "Inde, Ambuye, cukanga agalu amadyako nyenyenswa yuponela pa tebulo yamene ana adyelapo."