\v 5 Afalisi ndi alembi anamufunsa Yesu, " Kodi niciani wophumzila anu sakonkha mwambo wa makolo, cifukwa alikudya buledi wosasamba kumanja?"