\v 36 Ndipo analamlila iwo kuti asauze munthu aliyense. Koma mwamene iye analikuwalesa kuuza ene, ambiri analakhula. \v 37 Anali wodabwa kwambiri, ndi kunena, " Acita vintu vonse bwino. Alikupanga cukanga wosamvela kuyamba kumva ndi ababa ali kulankhula."