\v 37 Anabwelela ndipo anapeza iwo kuti aligone, ndipo anati kwa Petulo, "Simoni, kodi ulikugona? Kodi sungayembekezeko cabe kwa ola imodzi? \v 38 Wona ndikupemphela kuti usangene mumayeselo. Mzimu ulikufuna koma thupi ya lema." \v 39 Anayendatso patsogolo kukapemphela, ndipo anabwezelapo mau amodzi- amodzi.