ny_mrk_text_reg/07/17.txt

2 lines
380 B
Plaintext
Raw Normal View History

\v 17 Manje pamene Yesu anacoka pa anthu ambiri anangena mnyumba, wophunzila ake anamfunsa pafanizo.
\v 18 Yesu anati, " Kodi inunso muli wopanda mamveselo? simuona inu kuti camene cingena m'munthu kucokela kunja sicingadese munthu, \v 19 cifukwa siciyenda mkati mwa mtima, koma cimayenda m'mala ndikupita ku ciphuzi?" pali ici Yesu anatanthauza kuti cakudya cili conse nicoyela.