1 line
356 B
Plaintext
1 line
356 B
Plaintext
\v 15 Yoswa na Israyeli bonse banalekelela kuti bagonjesewe pamenso pao, na kuthabila ku cipululi. \v 16 Onse bantu banali mu mzinda banaitaniwa kuti ba pepeke, ndipo banapepeka Yoswa nakucosewako ku muzinda. \v 17 Kulibe munthu alibonse anasalila mu Ai na Beteli amene anayenda kupepeka Israyeli. Banasiya muzi kopanda aliyense pamene banapepeka Israyeli. |