|
\v 20 Pamene banaliza mphalasa na malupenga, bantu banapunda maningi navipupa vinagwa pansi. Ndipo mwa muna aliyense anayenda mukati nakutenga muzinda. \v 21 Banaongelatu vonse mumzinda nalupanga - mwamuna na mkazi, mingono na mkulu, ng' mbe, nkhosa na abulu. |