1 line
403 B
Plaintext
1 line
403 B
Plaintext
\v 10 Tinamvela mwamene Yehova anayumisila manzi ya mu nyanja imwe pamene pamene munacoka ku Eigipito. Tinamvelanso vamene munacita kumafumu yabili yaku Amori kumbali ya Yolodani - sihoni na ogi - yamene munabonongelatu. \v 11 Mwamusanga pamene tinamvela mitima yathu yanasungunuka kunalibe na mphavu inasala muli ali bonse - popeza Yehova mulungu wanu, nimulungu wa mwamba kumwamba na paziko ya pansi. |