\v 6 Koma anabakwelesa pamwamba pamalata na kubabisa namitenga yamene anaika pamalata. \v 7 Ndipo bamuna anaba pepeka pa njira yopita ku Yolodani. Ciseko cinavalika pamene opepeka anacoka.