\v 20 Iye wakuchitira umboni bzinthu ibzi anilewa, ''Inde! Ndikubwera tsampanopa.'' Amen! Bwerani, Mbuya Yesu! \v 21 Chifundo cha Mbuya Yesu chikhale na wakuchena mtima wensene. Amen.