\v 16 Ine, Yesu ndatuma mnjero wangu kukuchitirani umboni bza ibzi mmipingo. Ndine muzi wa dzinza la Davide, nyenyezi yakutoya ya kumachibese.