Thu Feb 15 2024 14:01:31 GMT+0200 (Central Africa Time)

This commit is contained in:
tsDesktop 2024-02-15 14:01:31 +02:00
parent bdd5c69ce5
commit fd7b5a3b8f
2 changed files with 3 additions and 2 deletions

View File

@ -1 +1 @@
\v 15 \v 16 \v 17 Nathangwe limweri, ali pamaso pa mpando wachifumu wa Mulungu, apo ambamunamata masikati na usiku mu kachisi wache. Iye wakukhala pampando wachifumu amdzawachitira iwo mnthunzi. Amdzakhala lini pomwe na njala, ayai kudzabva pomwe nyota. Dzuwa limdzawatenthalini ayai chithuthu chirichense. Thangwe Mwana wabira pakati nakati pa mpando wachifumiu amdzawafuwa achidzawatsogolera ku akasupe wa madzi ya moyo, apo Mulungu amdzapukusa misozi yensene kuchoka mmaso mwao.''
\v 15 Nathangwe limweri, ali pamaso pa mpando wachifumu wa Mulungu, apo ambamunamata masikati na usiku mu kachisi wache. Iye wakukhala pampando wachifumu amdzawachitira iwo mnthunzi. \v 16 Amdzabva lini pomwe na njala, ayai kudzabva pomwe nyota. Dzuwa limdzawatenthalini ayai chithuthu chirichense. \v 17 Thangwe Mwana wabira pakati nakati pa mpando wachifumu amdzawafuwa achidzawatsogolera ku akasupe wa madzi ya moyo, apo Mulungu amdzapukusa misozi yensene kuchoka mmaso mwao.''

View File

@ -98,6 +98,7 @@
"07-07",
"07-09",
"07-11",
"07-13"
"07-13",
"07-15"
]
}