Wed Feb 14 2024 16:20:35 GMT+0200 (Central Africa Time)

This commit is contained in:
tsDesktop 2024-02-14 16:20:36 +02:00
parent 2dc82bec64
commit 0147d873d4
2 changed files with 3 additions and 2 deletions

View File

@ -1 +1 @@
Pomwe Mwana wabira adatsudzula chizindikiro chachinayi, ndidabva mafala ya chamoyo chachinayi kulewa kuti, ''Bwerani!'' Kinangoka ndidaona kavalo yapfumbu. Wakuipakirayo dzina lache Imfa, apo Hade ikhamutewera. Iwo adapasiwa ulamuliro pambuto yakukula kuti ingapite kanayi mdziko lapansi, na njala na matenda, na nyama zakutengo zapadziko lapansi.
\v 7 Pomwe Mwana wabira adatsudzula chizindikiro chachinayi, ndidabva mafala ya chamoyo chachinayi kulewa kuti, ''Bwerani!'' \v 8 Kinangoka ndidaona kavalo yapfumbu. Wakuipakirayo dzina lache Imfa, apo Hade ikhamutewera. Iwo adapasiwa ulamuliro pambuto yakukula kuti ingapite kanayi mdziko lapansi, bwakupha na dipa, na njala na matenda, na nyama zakuthengo zapadziko lapansi.

View File

@ -87,6 +87,7 @@
"06-title",
"06-01",
"06-03",
"06-05"
"06-05",
"06-07"
]
}