nyu-ml-nyungwe_mat_text_reg/18/10.txt

1 line
192 B
Plaintext

\v 10 \v 11 Onesesani kuti nampodi kupepusa m'bodzi wa ang'ono ang'ono awa. Nakuti nilewa kuna imwe kuti kudzaulu anjero wawo nthawi zense ambayang'ana pankhope pa Babangu ndiye ali ku dzaulu.