nyu-ml-nyungwe_mat_text_reg/05/21.txt

1 line
447 B
Plaintext

\v 21 ''Mwabva kuti kudalewedwa kwa iwo kalekalelo, 'Nampodi kupha.' ndipo, 'Aliyense wa kupha anzakhala pa mpholemphole ya chiweruzo.' \v 22 Koma ndikulewa kwa imwe kuti aliyense omwe wakukalipiwa m'bale wache ali pa mphole yakutambira chilango; ndipo omwe anilimula m'bale wache kuti, 'Ndiwe wa pezipezi!' anzalakhala pa chigopsero cha kutongiwa; ndipo ule wakulewa kuti, 'Iwe chilema!' anzakhala pa chigopsero cha kudzayenda ku ng'anjo ya moto.