nyu-ml-nyungwe_mat_text_reg/27/51.txt

1 line
364 B
Plaintext

\v 51 Onani, chinguwo cha mtchalitchi chidang'ambika pawiri kuchokera padzaulu ate panyansi, apo dziko lapansi lidatekenyeka, apo mathanthwe yaching'ambika pakati. \v 52 Nthutu zidafukuka padecha, apo mathupi ya anyamuya wakulemekezeka yadalamusiwa. \v 53 Adabula kuchoka mu nthutu zire iye atalamusiwa, nkupita mu mzinda wakulemekezeka, achionekera kuna azinji.