nyu-ml-nyungwe_mat_text_reg/05/21.txt

1 line
450 B
Plaintext

\v 21 ''Mwabva kuti kudalewedwa kwa iwo kalekalelo, 'Nampodi kupha.' ndipo, 'Aliyense wa kupha anzakhala pa mpholemphole ya chiweruzo.' \v 22 Soma ndikulewa kuna imwe kuti aliyense wakukalipira m'bale wache ali pa mpholemphole yakutambira chilango; ndipo omwe anilimula m'bale wache kuti, 'Ndiwe wa pezipezi!' amdzalakhala pa chigopsero cha kutongiwa; ndipo ule wakulewa kuti, 'Iwe chilema!' anzakhala pa chigopsero cha kudzayenda ku ng'anjo ya moto.