\v 27 ''Mwabva kuti kudalewedwa, 'Nampodi kuyenda kumalume yaku mphasa.' \v 28 Koma ndikulewa kwa imwe kuti aliyense wakuyang'ana mkazi achimu khumba kugons naye wachita naye kale chigololo mumtima mwache.