\v 17 Panthawiyo Yesu adayamba kupfunzisa achiti, ''Lapani, pakuti ufumu bwa kudzaulu bwafendela.''