\v 18 ''Nyang'anani, kapolo wangu omwe ndidamusankhula; nyakukondewayo, mwa iye mzimu wangu unidekedwa naye. Nimdzaikha Mzimu wangu pana iye, apo iye amdzalalikira chilungamo kuna Wachikunja.