Thu Nov 16 2023 19:27:41 GMT+0200 (Central Africa Time)

This commit is contained in:
tsDesktop 2023-11-16 19:27:42 +02:00
parent 87cebc669a
commit 8ad05e534f
1 changed files with 1 additions and 1 deletions

View File

@ -1 +1 @@
\v 51 \v 52 \v 53 Onani, chinguwo cha mtchalitchi chidang'ambika pawiri kuchokera padzaulu ate panyansi, apo dziko lapansi lidatekenyeka, apo mathanthwe yaching'ambika pakati. Nthutu zidafukuka padecha, apo mathupi ya anyamuya wakulemekezeka yadalamusiwa. Adabula kuchoka mu nthutu iye atalamusiwa, nkupita mu mzinda wakulemekezeka, achionekera kuna azinji.
\v 51 \v 52 \v 53 Onani, chinguwo cha mtchalitchi chidang'ambika pawiri kuchokera padzaulu ate panyansi, apo dziko lapansi lidatekenyeka, apo mathanthwe yaching'ambika pakati. Nthutu zidafukuka padecha, apo mathupi ya anyamuya wakulemekezeka yadalamusiwa. Adabula kuchoka mu nthutu zire iye atalamusiwa, nkupita mu mzinda wakulemekezeka, achionekera kuna azinji.