Thu Nov 16 2023 20:16:07 GMT+0200 (Central Africa Time)

This commit is contained in:
tsDesktop 2023-11-16 20:16:07 +02:00
parent 38faa66d39
commit 4a0b630cd5
1 changed files with 1 additions and 1 deletions

View File

@ -1 +1 @@
Yosefe adatenga thupilo achilikulunga mu nguwo yabwino, achikaliikha mu gwinza lache lachendilo akhadaligoba ku thanthwe. Kinangoka adagubuduza chi
Yosefe adatenga thupilo achilikulunga mu nguwo yabwino, achikaliikha mu gwinza lache lachendilo akhadaligoba ku thanthwe. Kinangoka adagubuduza chimwala achifunga mkuyenda. Maria Magadalene na Mariya winango ule adakhala popo basi