Thu Nov 23 2023 06:34:37 GMT+0200 (Central Africa Time)

This commit is contained in:
tsDesktop 2023-11-23 06:34:38 +02:00
parent c75a1a9b76
commit 28147181a8
1 changed files with 1 additions and 1 deletions

View File

@ -1 +1 @@
\v 5 Pambuyo pache Satana adamutengera munzinda wakuchena mkukamuyimisa pakatolotolo pa tchalitchi, \v 6 apo adati kuna iye , ''Penu ndiwe mwana wa mulungu bzithuse wekha pansi, pakuti, kudanembiwa, 'anzawuza angelo wache kuti akukonkhobze, ndipo anzakunyamula nzaulu m'manja mwawo, kuti miyendo yanu ingadzongeke na minyala.'''
\v 5 Pambuyo pache Satana adamutengera munzinda wakuchena mkukamuyimisa pakatolotolo pa tchalitchi, \v 6 apo adati kuna iye , ''Penu ndiwe mwana wa mulungu bzithuse wekha pansi, nakuti, kudanembiwa, 'amdzauza anjelo wache kuti akukonkhobze, apo anzakunyamula mdzaulu m'manja mwawo, kuti miyendo yako nampodi idzadzongeke na minyala.'''