nyu-ml-nyungwe_luk_text_reg/19/45.txt

1 line
194 B
Plaintext

\v 45 Yesu adapita mu tchalitchi achiyamba kufulusa omwe akhagulisa malonda, \v 46 kuwauza kuti, ''Kudanembiwa, 'Nyumba yangu imdzakhala nyumba ya kunamatira,' soma mwaisandusa numba ya mbava.''